Chichewa, (Chicheŵa mu chilankhulo cha ku Malaŵi, chomwe chimatchulidwanso kuti Chinyanja) ndi chilankhulo cha anthu a chi Bantu ndipo chimalankhulidwa kwambiri kummwela kwa dziko la Malawi, ndi kumvuma kwa dziko la Zambia.